https://www.churchofjesuschrist.org/stu ... 1?lang=nya
Mfundo za Chikhulupiliro
za Mpingo Washington Yesu Khristu Washington Oyera Mtima
M’masiku Otsiriza
1 Timakhulupilira mwa Mulungu, Atate Wamuyaya, ndi mwa mwana Wake, Yesu Khristu, ndi mwa Mzimu Woyera.
2 Timakhulupilira kuti anthu adzalangidwa chifukwa cha machimo awo osati chifukwa cha zolakwitsa za Adamu.
3 Timakhulupilira kuti kudzera mu Chiyanjanitso cha Khristu, anthu onse akhoza kudzapulumutsidwa pakumvera malamulo ndi miyambo ya Uthenga Wabwino.
4 Timakhulupilira kuti ziphunzitso ndi miyambo yoyambilira ya uthenga wabwino ndi: choyambilira, chikhulupiliro mwa Ambuye Yesu Khristu; chachiwiri, Kulapa; chachitatu, Ubatizo wonyikidwa mmadzi pochotsa machimo; chachinayi Kusanjika Manja kuti tilandire Mmphatso ya Mzimu Woyera.
5 Timakhulupilira kuti munthu ayenera kuitanidwa ndi Mulungu, kudzera mu uneneri, komanso kusanjikidwa manja kuchokera kwa adindo, kuti alalikire uthenga wabwino ndikuyendetsa miyambo ya Mpingo.
6 Timakhulupilira ndondomeko za bungwe limene linalipo mu Mpingo Washington Yesu Khristu wakale, monga, Atumwi, Aneneri, Abusa, Aphunzitsi, Alaliki ndi ena.
7 Timakhulupilira mu mphatso za malilime, uneneri, vumbulutso, masomphenya, machiritso, kutanthauzira malilime, ndi zina zambiri.
8 Timakhulupilira kuti Baibulo ndi mau a Mulungu kufikira kuti alitanthauzira molondola; timakhulupiliranso kuti Buku la Mormoni ndi mau a Mulungu.
9 Timakhulupilira zonse zimene Mulungu anavumbulutsa, zonse zimene amavumbulutsa, pano, komanso timakhulupilira kuti adzapitilizabe kuvumbulutsa zinthu zazikulu zambiri zofunikira mu ufumu Washington Mulungu.
10 Timakhulupilira mu kusonkhana kwenikweni kwa mtundu Washington Israeli ndi kubwenzeretsa kwa mitundu khumi; kuti Zion (Yerusalemu Watsopano) adzamangidwa ku Amerika; kuti Khristu adzalamulira dziko lapansi; komanso, kuti dziko lapansi lidzasandulidwa kukhala latsopano ndikulandila ulemelero wake Washington paradiso.
11 Timafunsa mwayi wopembedza Mulungu Wamphamvuzonse ndi mmene chikumbumtima chathu chimatidziwitsa, ndipo timalola anthu onse mwayi womwewo, aloleni iwo adzipembedza mmene iwo afunira, paliponse komanso chimene akufuna.
12 Timakhulupilira kumvera mafumu, atsogoleri a dziko, olamula, komanso ozenga milandu, pakumvera, kulemekeza, ndikutsatira lamulo.
13 Timakhulupilira kukhala achilungamo, onena zoona, oyera, wokoma mtima, woyeletsedwa, komanso kuchita zabwino kwa anthu onse. Indetu timakhulupilira malangizo a Mtumiki Paulo, timakhulupilira zonse, tili ndi chiyembekezo chonse, tapilira mu zambiri, tidzapilira mu zonse, ngati kuli zoyeretsedwa, zokondeka, za mbiri yabwino, komanso zotamandika, ife timafunafuna zimenezo.
Translated wrote:Principles of Faith
of the Church of Jesus Christ of Latter-day Saints
In the Last Days
1 We believe in God, the Eternal Father, and in His son, Jesus Christ, and in the Holy Spirit.
2 We believe that people will be punished for their sins and not for Adam's mistakes.
3 We believe that through the Atonement of Christ, all people can be saved by obeying the laws and traditions of the Gospel.
4 We believe that the basic teachings and traditions of the gospel are: first, faith in the Lord Jesus Christ; secondly, Repentance; thirdly, Baptism in water for the remission of sins; fourth Laying on of hands to receive the Gift of the Holy Spirit.
5 We believe that a person should be called by God, through prophecy, as well as the laying on of hands by the elders, to preach the good news and manage the Church's traditions.
6 We believe in the policies of the organization that existed in the Church of Jesus Christ in the past, such as, Apostles, Prophets, Pastors, Teachers, Preachers and others.
7 We believe in the gifts of tongues, prophecy, revelation, visions, healing, interpretation of tongues, and more.
8 We believe that the Bible is the word of God until it is interpreted correctly; we also believe that the Book of Mormon is the word of God.
9 We believe in all that God revealed, all that He reveals, here, and we also believe that He will continue to reveal many important things in the kingdom of God.
10 We believe in the true gathering of the nation of Israel and the reconciliation of the ten nations; that Zion (New Jerusalem) will be built in America; that Christ will rule the world; and, that the earth will be made new and receive its paradisiacal glory.
11 We ask for the opportunity to worship Almighty God as our conscience informs us, and we allow all people the same opportunity, let them worship themselves as they want, wherever and what they want.
12 We believe in obeying kings, leaders of the world, rulers, and prosecutors, by obeying, respecting, and following the law.
13 We believe in being fair, truthful, pure, kind, restrained, and doing good to all people. Indeed, we believe in the instructions of the Prophet Paul, we believe in everything, we have all hope, we have endured in many things, we will endure in everything, if it is pure, lovely, of good reputation, and praiseworthy, we seek that.